The Quran in Chichewa - Surah Fatiha translated into Chichewa, Surah Al-Fatihah in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Fatiha in Chichewa - نيانجا, Verses 7 - Surah Number 1 - Page 1.
بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ (1) M’dzina la Mulungu, Mwini Chifundo ndi Mwini Chisoni Chosatha |
الْحَمْدُ لِلَّهِ رَبِّ الْعَالَمِينَ (2) Kuyamikidwandikwa Mulungu,Ambuyewachilengedwe |
الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ (3) Mwini Chifundo ndi Mwini Chisoni Chosatha |
مَالِكِ يَوْمِ الدِّينِ (4) Mfumu ya tsiku la Chiweruzo |
إِيَّاكَ نَعْبُدُ وَإِيَّاكَ نَسْتَعِينُ (5) Inu nokha tikulambirani ndipo ndi kwa Inu nokha kumene timapempha chithandizo |
اهْدِنَا الصِّرَاطَ الْمُسْتَقِيمَ (6) Tilangizeni njira yanu yoyenera |
صِرَاطَ الَّذِينَ أَنْعَمْتَ عَلَيْهِمْ غَيْرِ الْمَغْضُوبِ عَلَيْهِمْ وَلَا الضَّالِّينَ (7) Njira ya iwo amene mwawakonda osati ya iwo amene adalandira mkwiyo wanu kapena anasokera |