The Quran in Chichewa - Surah Falaq translated into Chichewa, Surah Al-Falaq in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Falaq in Chichewa - نيانجا, Verses 5 - Surah Number 113 - Page 604.
قُلْ أَعُوذُ بِرَبِّ الْفَلَقِ (1) Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa M’mbandakucha |
مِن شَرِّ مَا خَلَقَ (2) Kuchokera ku zinthu zonyansa zimene walenga |
وَمِن شَرِّ غَاسِقٍ إِذَا وَقَبَ (3) Ndi kuchokera ku zonyansa za nthawi ya usiku pamene mdima ufika |
وَمِن شَرِّ النَّفَّاثَاتِ فِي الْعُقَدِ (4) Ndi kuchokera ku zonyansa za anthu a matsenga pamene auzila pfundo |
وَمِن شَرِّ حَاسِدٍ إِذَا حَسَدَ (5) “Ndi ku zonyansa za munthu wa dumbo pamene achita nsanje.” |