The Quran in Chichewa - Surah An Nas translated into Chichewa, Surah An-Nas in Chichewa. We provide accurate translation of Surah An Nas in Chichewa - نيانجا, Verses 6 - Surah Number 114 - Page 604.
قُلْ أَعُوذُ بِرَبِّ النَّاسِ (1) Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa anthu |
مَلِكِ النَّاسِ (2) Mfumu ya anthu |
إِلَٰهِ النَّاسِ (3) Mulungu wa anthu |
مِن شَرِّ الْوَسْوَاسِ الْخَنَّاسِ (4) Kuchokera ku zonyansa za kazitape amene amachoka akatha |
الَّذِي يُوَسْوِسُ فِي صُدُورِ النَّاسِ (5) Amene amanong’oneza m’mitima mwa anthu |
مِنَ الْجِنَّةِ وَالنَّاسِ (6) Ya majini ndi anthu.” |