The Quran in Chichewa - Surah Al Asr translated into Chichewa, Surah Al-Asr in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Al Asr in Chichewa - نيانجا, Verses 3 - Surah Number 103 - Page 601.
وَالْعَصْرِ (1) Pali nthawi |
إِنَّ الْإِنسَانَ لَفِي خُسْرٍ (2) Ndithudi ! Munthu ndi otayika |
إِلَّا الَّذِينَ آمَنُوا وَعَمِلُوا الصَّالِحَاتِ وَتَوَاصَوْا بِالْحَقِّ وَتَوَاصَوْا بِالصَّبْرِ (3) Kupatula okhawo amene amakhulupirira ndi kuchita ntchito zabwino ndipo amalimbikitsana wina ndi mzake kuchita chilungamo ndi kukumbutsana kupirira |