The Quran in Chichewa - Surah Nasr translated into Chichewa, Surah An-Nasr in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Nasr in Chichewa - نيانجا, Verses 3 - Surah Number 110 - Page 603.
إِذَا جَاءَ نَصْرُ اللَّهِ وَالْفَتْحُ (1) Pamene chithandizo cha Mulungu chidza ndi kupambana |
وَرَأَيْتَ النَّاسَ يَدْخُلُونَ فِي دِينِ اللَّهِ أَفْوَاجًا (2) Ndipo uona anthu akulowa m’chipembedzo cha Mulungu mu unyinji wawo |
فَسَبِّحْ بِحَمْدِ رَبِّكَ وَاسْتَغْفِرْهُ ۚ إِنَّهُ كَانَ تَوَّابًا (3) Motero lemekeza Ambuye wako ndipo upemphe chikhululukiro chake. Ndithudi Iye amavomera kulapa ndipo ndi wokhululukira |