Quran with Chichewa translation - Surah An-Nasr ayat 3 - النَّصر - Page - Juz 30
﴿فَسَبِّحۡ بِحَمۡدِ رَبِّكَ وَٱسۡتَغۡفِرۡهُۚ إِنَّهُۥ كَانَ تَوَّابَۢا ﴾
[النَّصر: 3]
﴿فسبح بحمد ربك واستغفره إنه كان توابا﴾ [النَّصر: 3]
Khaled Ibrahim Betala “Pamenepo lemekeza Mbuye wako ndi kumtamanda ndiponso mpemphe chikhululuko, ndipo ndithu Iye ndiwolandira mochuluka kulapa (kwa anthu Ake) |