The Quran in Chichewa - Surah Kafirun translated into Chichewa, Surah Al-Kafirun in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Kafirun in Chichewa - نيانجا, Verses 6 - Surah Number 109 - Page 603.
قُلْ يَا أَيُّهَا الْكَافِرُونَ (1) Nena: oh! Inu anthu osakhulupirira |
لَا أَعْبُدُ مَا تَعْبُدُونَ (2) Ine sindipembedza chimene inu mupembedza |
وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ (3) Ndiponso inu simudzapembedza chimene ine ndipembedza |
وَلَا أَنَا عَابِدٌ مَّا عَبَدتُّمْ (4) Ndipo ine sindidzapembedza chimene inu muli kuchipembedza |
وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ (5) Ndipo inu simudzapembedza chimene ine ndimapembedza |
لَكُمْ دِينُكُمْ وَلِيَ دِينِ (6) Kwa inu chipembedzo chanu ndipo kwa ine chipembedzo changa |