The Quran in Chichewa - Surah Sharh translated into Chichewa, Surah Ash-Sharh in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Sharh in Chichewa - نيانجا, Verses 8 - Surah Number 94 - Page 596.

| أَلَمْ نَشْرَحْ لَكَ صَدْرَكَ (1) Kodi Ife sitidatsegule chifuwa chako |
| وَوَضَعْنَا عَنكَ وِزْرَكَ (2) Ndi kukuchotsa katundu wako wolemera |
| الَّذِي أَنقَضَ ظَهْرَكَ (3) Amene amalemetsa msana wako |
| وَرَفَعْنَا لَكَ ذِكْرَكَ (4) Ndipo tidakweza mbiri yako yabwino |
| فَإِنَّ مَعَ الْعُسْرِ يُسْرًا (5) Ndithudi m’mavuto muli chithandizo |
| إِنَّ مَعَ الْعُسْرِ يُسْرًا (6) Ndithudi m’mavuto muli chithandizo |
| فَإِذَا فَرَغْتَ فَانصَبْ (7) Ndipo pamene wamaliza, pembedza Mulungu |
| وَإِلَىٰ رَبِّكَ فَارْغَب (8) Ndipo dzipereke kwathunthu kwa Ambuye wako |