The Quran in Chichewa - Surah Tin translated into Chichewa, Surah At-Tin in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Tin in Chichewa - نيانجا, Verses 8 - Surah Number 95 - Page 597.

| بِّسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ وَالتِّينِ وَالزَّيْتُونِ (1) Pali mtengo wa mkuyu ndi mtengo wa azitona | 
| وَطُورِ سِينِينَ (2) Ndi pali phiri la Sinai | 
| وَهَٰذَا الْبَلَدِ الْأَمِينِ (3) Ndi pali Mzinda uwu wa mtendere | 
| لَقَدْ خَلَقْنَا الْإِنسَانَ فِي أَحْسَنِ تَقْوِيمٍ (4) Ndithudi Ife tidamulenga munthu m’chikombole chabwino | 
| ثُمَّ رَدَدْنَاهُ أَسْفَلَ سَافِلِينَ (5) Ndipo tinamutsitsa kukhala wapansi zedi | 
| إِلَّا الَّذِينَ آمَنُوا وَعَمِلُوا الصَّالِحَاتِ فَلَهُمْ أَجْرٌ غَيْرُ مَمْنُونٍ (6) Kupatula amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, iwo adzalandira mphotho yosatha | 
| فَمَا يُكَذِّبُكَ بَعْدُ بِالدِّينِ (7) Kodi ndi chiyani, chimene chili kukupangitsani kukana tsiku la chiweruzo | 
| أَلَيْسَ اللَّهُ بِأَحْكَمِ الْحَاكِمِينَ (8) Kodi Mulungu si woweruza wabwino kuposa oweruza onse |