Quran with Chichewa translation - Surah At-Tin ayat 7 - التِّين - Page - Juz 30
﴿فَمَا يُكَذِّبُكَ بَعۡدُ بِٱلدِّينِ ﴾
[التِّين: 7]
﴿فما يكذبك بعد بالدين﴾ [التِّين: 7]
Khaled Ibrahim Betala “Tsono nchiyani chakuchititsa kuti ukanire kuuka ndi malipiro pambuyo (poona mphamvu zathu pa chilichonse) |