The Quran in Chichewa - Surah Qadr translated into Chichewa, Surah Al-Qadr in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Qadr in Chichewa - نيانجا, Verses 5 - Surah Number 97 - Page 598.
بِّسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ إِنَّا أَنزَلْنَاهُ فِي لَيْلَةِ الْقَدْرِ (1) Ndithudi tinavumbulutsa ilo mu usiku wamphamvu |
وَمَا أَدْرَاكَ مَا لَيْلَةُ الْقَدْرِ (2) Kodi ndi chiyani chimene chingakuuzeni kuti mudziwe kuti usiku wamphamvu ndi otani |
لَيْلَةُ الْقَدْرِ خَيْرٌ مِّنْ أَلْفِ شَهْرٍ (3) Usiku wamphamvu ndi wabwino kuposa miyezi chikwi chimodzi |
تَنَزَّلُ الْمَلَائِكَةُ وَالرُّوحُ فِيهَا بِإِذْنِ رَبِّهِم مِّن كُلِّ أَمْرٍ (4) Mu usiku umenewu Angelo ndi Mzimu, ndi chilolezo cha Mulungu, amachoka kumwamba ndi kutsika pansi ndi malamulo ake onse |
سَلَامٌ هِيَ حَتَّىٰ مَطْلَعِ الْفَجْرِ (5) Mtendere mpaka m’mbandakucha |