القرآن باللغة نيانجا - سورة القدر مترجمة إلى اللغة نيانجا، Surah Qadr in Chichewa. نوفر ترجمة دقيقة سورة القدر باللغة نيانجا - Chichewa, الآيات 5 - رقم السورة 97 - الصفحة 598.

| بِّسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ إِنَّا أَنزَلْنَاهُ فِي لَيْلَةِ الْقَدْرِ (1) Ndithudi tinavumbulutsa ilo mu usiku wamphamvu | 
| وَمَا أَدْرَاكَ مَا لَيْلَةُ الْقَدْرِ (2) Kodi ndi chiyani chimene chingakuuzeni kuti mudziwe kuti usiku wamphamvu ndi otani | 
| لَيْلَةُ الْقَدْرِ خَيْرٌ مِّنْ أَلْفِ شَهْرٍ (3) Usiku wamphamvu ndi wabwino kuposa miyezi chikwi chimodzi | 
| تَنَزَّلُ الْمَلَائِكَةُ وَالرُّوحُ فِيهَا بِإِذْنِ رَبِّهِم مِّن كُلِّ أَمْرٍ (4) Mu usiku umenewu Angelo ndi Mzimu, ndi chilolezo cha Mulungu, amachoka kumwamba ndi kutsika pansi ndi malamulo ake onse | 
| سَلَامٌ هِيَ حَتَّىٰ مَطْلَعِ الْفَجْرِ (5) Mtendere mpaka m’mbandakucha |