Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kauthar ayat 2 - الكَوثر - Page - Juz 30
﴿فَصَلِّ لِرَبِّكَ وَٱنۡحَرۡ ﴾
[الكَوثر: 2]
﴿فصل لربك وانحر﴾ [الكَوثر: 2]
Khaled Ibrahim Betala “(Pakuti ndakupatsa zimenezo), pitiriza kupembedza Mbuye wako (moyera mtima) ndipo ipha nsembe yako (chifukwa chakuthokoza Allah pa zimene wakupatsa, monga ulemelero ndikukusankhira zabwino zambiri) |