The Quran in Chichewa - Surah Kawthar translated into Chichewa, Surah Al-Kawthar in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Kawthar in Chichewa - نيانجا, Verses 3 - Surah Number 108 - Page 602.
إِنَّا أَعْطَيْنَاكَ الْكَوْثَرَ (1) Ndithudi takupatsa iwe Mtsinje wa Paradiso |
فَصَلِّ لِرَبِّكَ وَانْحَرْ (2) Motero pemphera chifukwa cha Ambuye wako ndipo upereke nsembe |
إِنَّ شَانِئَكَ هُوَ الْأَبْتَرُ (3) Ndithudi aliyense amene akukwiyitsa iwe adzakhala wopanda choyembekezera |