Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 27 - طه - Page - Juz 16
﴿وَٱحۡلُلۡ عُقۡدَةٗ مِّن لِّسَانِي ﴾
[طه: 27]
﴿واحلل عقدة من لساني﴾ [طه: 27]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndipo masulani mfundo yomwe ili ku lirime kwanga, (ndimasulireni kumangika kwa lirime langa kuti mawu anga akakhale opanda chibwibwi).” |