Quran with Chichewa translation - Surah Al-Muddaththir ayat 7 - المُدثر - Page - Juz 29
﴿وَلِرَبِّكَ فَٱصۡبِرۡ ﴾
[المُدثر: 7]
﴿ولربك فاصبر﴾ [المُدثر: 7]
Khaled Ibrahim Betala “Chifukwa cha Mbuye wako, pirira (ku malamulo Ake poleka zomwe waletsa ndi kuchita zimene walamula) |