Quran with Chichewa translation - Surah An-Naba’ ayat 15 - النَّبَإ - Page - Juz 30
﴿لِّنُخۡرِجَ بِهِۦ حَبّٗا وَنَبَاتٗا ﴾
[النَّبَإ: 15]
﴿لنخرج به حبا ونباتا﴾ [النَّبَإ: 15]
Khaled Ibrahim Betala “Kuti titulutse ndi madziwo mbewu ndi m’mera, (chomwe ndi chakudya cha anthu ndi nyama) |