Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shams ayat 5 - الشَّمس - Page - Juz 30
﴿وَٱلسَّمَآءِ وَمَا بَنَىٰهَا ﴾ 
[الشَّمس: 5]
﴿والسماء وما بناها﴾ [الشَّمس: 5]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndi thambo ndi (Mwini mphamvu zonse Wamkulu) Yemwe adalimanga ndi kulitukula (mwaluso) |