The Quran in Chichewa - Surah Adiyat translated into Chichewa, Surah Al-Adiyat in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Adiyat in Chichewa - نيانجا, Verses 11 - Surah Number 100 - Page 599.

| وَالْعَادِيَاتِ ضَبْحًا (1) Palizothamangakwambirindikupumakwawokofulumira |
| فَالْمُورِيَاتِ قَدْحًا (2) Ndi zimene zimaonetsa moto zikamathamanga |
| فَالْمُغِيرَاتِ صُبْحًا (3) Ndipo zimachita nkhondo m’mbandakucha |
| فَأَثَرْنَ بِهِ نَقْعًا (4) Ndi kuonetsa fumbi |
| فَوَسَطْنَ بِهِ جَمْعًا (5) Ndi kuphwanya pakati gulu la adani |
| إِنَّ الْإِنسَانَ لِرَبِّهِ لَكَنُودٌ (6) Ndithudi! Munthu sathokoza kwaAmbuye wake |
| وَإِنَّهُ عَلَىٰ ذَٰلِكَ لَشَهِيدٌ (7) Ndipo mwini wake amachitira umboni zimenezi |
| وَإِنَّهُ لِحُبِّ الْخَيْرِ لَشَدِيدٌ (8) Ndithudi iye ali kukonda chuma kwambiri |
| ۞ أَفَلَا يَعْلَمُ إِذَا بُعْثِرَ مَا فِي الْقُبُورِ (9) Kodi iye sadziwa kuti pamene zonse zili m’manda zidzatulutsidwa ndi kuonetsedwa poyera |
| وَحُصِّلَ مَا فِي الصُّدُورِ (10) Ndizonsezimenezilim’mitimayaanthuzizidzaululidwa |
| إِنَّ رَبَّهُم بِهِمْ يَوْمَئِذٍ لَّخَبِيرٌ (11) Ndithudi, patsiku limeneli, Ambuye wako adzakhala ali kudziwa chilichonse |