القرآن باللغة نيانجا - سورة العاديات مترجمة إلى اللغة نيانجا، Surah Adiyat in Chichewa. نوفر ترجمة دقيقة سورة العاديات باللغة نيانجا - Chichewa, الآيات 11 - رقم السورة 100 - الصفحة 599.
وَالْعَادِيَاتِ ضَبْحًا (1) Palizothamangakwambirindikupumakwawokofulumira |
فَالْمُورِيَاتِ قَدْحًا (2) Ndi zimene zimaonetsa moto zikamathamanga |
فَالْمُغِيرَاتِ صُبْحًا (3) Ndipo zimachita nkhondo m’mbandakucha |
فَأَثَرْنَ بِهِ نَقْعًا (4) Ndi kuonetsa fumbi |
فَوَسَطْنَ بِهِ جَمْعًا (5) Ndi kuphwanya pakati gulu la adani |
إِنَّ الْإِنسَانَ لِرَبِّهِ لَكَنُودٌ (6) Ndithudi! Munthu sathokoza kwaAmbuye wake |
وَإِنَّهُ عَلَىٰ ذَٰلِكَ لَشَهِيدٌ (7) Ndipo mwini wake amachitira umboni zimenezi |
وَإِنَّهُ لِحُبِّ الْخَيْرِ لَشَدِيدٌ (8) Ndithudi iye ali kukonda chuma kwambiri |
۞ أَفَلَا يَعْلَمُ إِذَا بُعْثِرَ مَا فِي الْقُبُورِ (9) Kodi iye sadziwa kuti pamene zonse zili m’manda zidzatulutsidwa ndi kuonetsedwa poyera |
وَحُصِّلَ مَا فِي الصُّدُورِ (10) Ndizonsezimenezilim’mitimayaanthuzizidzaululidwa |
إِنَّ رَبَّهُم بِهِمْ يَوْمَئِذٍ لَّخَبِيرٌ (11) Ndithudi, patsiku limeneli, Ambuye wako adzakhala ali kudziwa chilichonse |