The Quran in Chichewa - Surah Quraysh translated into Chichewa, Surah Quraysh in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Quraysh in Chichewa - نيانجا, Verses 4 - Surah Number 106 - Page 602.
لِإِيلَافِ قُرَيْشٍ (1) Pofuna kuteteza mtundu wa Quraish |
إِيلَافِهِمْ رِحْلَةَ الشِّتَاءِ وَالصَّيْفِ (2) Kuti apitirire pa maulendo nthawi ya Chilimwe ndi m’nthawi ya Chisanu |
فَلْيَعْبُدُوا رَبَّ هَٰذَا الْبَيْتِ (3) Motero auzeni kuti azipembedza Ambuye wa Nyumba ino |
الَّذِي أَطْعَمَهُم مِّن جُوعٍ وَآمَنَهُم مِّنْ خَوْفٍ (4) Amene wawadyetsa m’masiku a njala ndi kuwachotsa mantha |