Quran with Chichewa translation - Surah Quraish ayat 2 - قُرَيش - Page - Juz 30
﴿إِۦلَٰفِهِمۡ رِحۡلَةَ ٱلشِّتَآءِ وَٱلصَّيۡفِ ﴾
[قُرَيش: 2]
﴿إيلافهم رحلة الشتاء والصيف﴾ [قُرَيش: 2]
Khaled Ibrahim Betala “Apitilize chizolowezi chawo choyenda nthawi ya dzinja (kunka ku Yemen) ndi nthawi yachirimwe (kunka ku Sham kukachita malonda, mosatekeseka ndi mopanda mantha) |