Quran with Chichewa translation - Surah Quraish ayat 4 - قُرَيش - Page - Juz 30
﴿ٱلَّذِيٓ أَطۡعَمَهُم مِّن جُوعٖ وَءَامَنَهُم مِّنۡ خَوۡفِۭ ﴾
[قُرَيش: 4]
﴿الذي أطعمهم من جوع وآمنهم من خوف﴾ [قُرَيش: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Yemwe amawadyetsa (nthawi imene Arabu anzawo) ali m’njala, ndipo amawapatsa chitetezo (pomwe anzawo) ali ndi mantha |