The Quran in Chichewa - Surah Maun translated into Chichewa, Surah Al-Maun in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Maun in Chichewa - نيانجا, Verses 7 - Surah Number 107 - Page 602.

| أَرَأَيْتَ الَّذِي يُكَذِّبُ بِالدِّينِ (1) Kodi wamuona munthu amene amakana kuti kuli tsiku la chiweruzo | 
| فَذَٰلِكَ الَّذِي يَدُعُّ الْيَتِيمَ (2) Iye ndiye amene amazunza mwana wamasiye | 
| وَلَا يَحُضُّ عَلَىٰ طَعَامِ الْمِسْكِينِ (3) Ndipo sakakamiza anthu ena kuti azidyetsa anthu osauka | 
| فَوَيْلٌ لِّلْمُصَلِّينَ (4) Motero tsoka kwa iwo amene amapemphera | 
| الَّذِينَ هُمْ عَن صَلَاتِهِمْ سَاهُونَ (5) Amene salabadira mapemphero awo | 
| الَّذِينَ هُمْ يُرَاءُونَ (6) Amene amachita zabwino pofuna kuti ena awaone | 
| وَيَمْنَعُونَ الْمَاعُونَ (7) Ndipo amakana kupereka chaulere |