Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kafirun ayat 6 - الكافِرون - Page - Juz 30
﴿لَكُمۡ دِينُكُمۡ وَلِيَ دِينِ ﴾
[الكافِرون: 6]
﴿لكم دينكم ولي دين﴾ [الكافِرون: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Inu muli ndi chipembedzo chanu (chimene mukuchikhulupirira), inenso ndili ndi chipembedzo changa (chimene Allah wandisankhira) |