Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 1 - النَّمل - Page - Juz 19
﴿طسٓۚ تِلۡكَ ءَايَٰتُ ٱلۡقُرۡءَانِ وَكِتَابٖ مُّبِينٍ ﴾
[النَّمل: 1]
﴿طس تلك آيات القرآن وكتاب مبين﴾ [النَّمل: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Tâ-Sîn. Izi ndi Ayah (ndime) (za Qur’an buku lodzazidwa ndi zothandiza), ndiponso buku lofotokoza (chilichonse chauzimu ndi chamoyo wadziko) |