Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 5 - الرُّوم - Page - Juz 21
﴿بِنَصۡرِ ٱللَّهِۚ يَنصُرُ مَن يَشَآءُۖ وَهُوَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلرَّحِيمُ ﴾
[الرُّوم: 5]
﴿بنصر الله ينصر من يشاء وهو العزيز الرحيم﴾ [الرُّوم: 5]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi chithandizo cha Allah (chimene iwo adzapatsidwa, chomwe ndikugonjetsa Aquraish tsiku lomwelo). (Allah) amamthandiza amene wamfuna, ndipo Iye Ngwamphamvu zoposa; Ngwachisoni chosatha |