Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 1 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿وَٱلصَّٰٓفَّٰتِ صَفّٗا ﴾
[الصَّافَات: 1]
﴿والصافات صفا﴾ [الصَّافَات: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Ndikulumbira (angelo) amene amandanda m’mizere yondondozana, (popembedza ndi kugonjera Mbuye wawo) |