Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 166 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿وَإِنَّا لَنَحۡنُ ٱلۡمُسَبِّحُونَ ﴾
[الصَّافَات: 166]
﴿وإنا لنحن المسبحون﴾ [الصَّافَات: 166]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndipo (ena mwa) ife ngolemekeza (Allah nthawi zonse ndi kumtamanda ndi kumpatula ku zinthu zosayenerana ndi ulemelero wake).” |