Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rahman ayat 63 - الرَّحمٰن - Page - Juz 27
﴿فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ﴾
[الرَّحمٰن: 63]
﴿فبأي آلاء ربكما تكذبان﴾ [الرَّحمٰن: 63]
Khaled Ibrahim Betala “(Inu zolengedwa za mitundu iwiri, anthu ndi ziwanda), kodi ndi mtendere uti wa Mbuye wanu umene mukuukana (kuti si Wake) |