Quran with Chichewa translation - Surah Al-Buruj ayat 14 - البُرُوج - Page - Juz 30
﴿وَهُوَ ٱلۡغَفُورُ ٱلۡوَدُودُ ﴾
[البُرُوج: 14]
﴿وهو الغفور الودود﴾ [البُرُوج: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Iye, ndi Wokhululuka (kwa amene walapa kwa Iye), ndiponso Wokonda kwambiri (amene akumkonda ndi kumumvera) |