Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma‘un ayat 6 - المَاعُون - Page - Juz 30
﴿ٱلَّذِينَ هُمۡ يُرَآءُونَ ﴾
[المَاعُون: 6]
﴿الذين هم يراءون﴾ [المَاعُون: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Amenenso (akamachita mapemphero awo) amadzionetsera (kwa anthu mwachipha maso kuti apeze ulemelero ndi kutamandidwa mmitima mwa anthu) |