Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma‘un ayat 7 - المَاعُون - Page - Juz 30
﴿وَيَمۡنَعُونَ ٱلۡمَاعُونَ ﴾
[المَاعُون: 7]
﴿ويمنعون الماعون﴾ [المَاعُون: 7]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amamana ziwiya (zawo posabwereka anzawo zinthu zofunika pa moyo wa aliyense monga nkhwangwa, mpeni, mtondo ndi zina zotere) |