القرآن باللغة نيانجا - سورة الماعون مترجمة إلى اللغة نيانجا، Surah Maun in Chichewa. نوفر ترجمة دقيقة سورة الماعون باللغة نيانجا - Chichewa, الآيات 7 - رقم السورة 107 - الصفحة 602.
أَرَأَيْتَ الَّذِي يُكَذِّبُ بِالدِّينِ (1) Kodi wamuona munthu amene amakana kuti kuli tsiku la chiweruzo |
فَذَٰلِكَ الَّذِي يَدُعُّ الْيَتِيمَ (2) Iye ndiye amene amazunza mwana wamasiye |
وَلَا يَحُضُّ عَلَىٰ طَعَامِ الْمِسْكِينِ (3) Ndipo sakakamiza anthu ena kuti azidyetsa anthu osauka |
فَوَيْلٌ لِّلْمُصَلِّينَ (4) Motero tsoka kwa iwo amene amapemphera |
الَّذِينَ هُمْ عَن صَلَاتِهِمْ سَاهُونَ (5) Amene salabadira mapemphero awo |
الَّذِينَ هُمْ يُرَاءُونَ (6) Amene amachita zabwino pofuna kuti ena awaone |
وَيَمْنَعُونَ الْمَاعُونَ (7) Ndipo amakana kupereka chaulere |