Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 9 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿وَٱلَّذِينَ هُمۡ عَلَىٰ صَلَوَٰتِهِمۡ يُحَافِظُونَ ﴾
[المؤمنُون: 9]
﴿والذين هم على صلواتهم يحافظون﴾ [المؤمنُون: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi omwe akusunga mapemphero awo (popemphera mu nthawi zake ndi kutsata malamulo ake uku ali odzichepetsa) |