Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 3 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿كِتَٰبٞ فُصِّلَتۡ ءَايَٰتُهُۥ قُرۡءَانًا عَرَبِيّٗا لِّقَوۡمٖ يَعۡلَمُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 3]
﴿كتاب فصلت آياته قرآنا عربيا لقوم يعلمون﴾ [فُصِّلَت: 3]
Khaled Ibrahim Betala “(Ili) ndi buku lomwe ma Ayah ake afotokozedwa (bwino pokhudza malamulo a zamdziko ndi tsiku lachimaliziro); chowerengedwa (chimene chavumbulutsidwa) m’chiyankhulo cha Chiarabu kwa anthu ozindikira (tsatanetsatane wa malamulo ake) |