×

Ndithudi talipanga Buku la Korani kukhala losavuta kulizindikira ndi kulikumbukira. Koma kodi 54:32 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qamar ⮕ (54:32) ayat 32 in Chichewa

54:32 Surah Al-Qamar ayat 32 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 32 - القَمَر - Page - Juz 27

﴿وَلَقَدۡ يَسَّرۡنَا ٱلۡقُرۡءَانَ لِلذِّكۡرِ فَهَلۡ مِن مُّدَّكِرٖ ﴾
[القَمَر: 32]

Ndithudi talipanga Buku la Korani kukhala losavuta kulizindikira ndi kulikumbukira. Koma kodi alipo ena amene adzachenjezedwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد يسرنا القرآن للذكر فهل من مدكر, باللغة نيانجا

﴿ولقد يسرنا القرآن للذكر فهل من مدكر﴾ [القَمَر: 32]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu taifewetsa Qur’an kuti ikhale chikumbutso. Kodi alipo woikumbukira (ndi kupeza nayo malangizo abwino)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek