Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rahman ayat 42 - الرَّحمٰن - Page - Juz 27
﴿فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ﴾ 
[الرَّحمٰن: 42]
﴿فبأي آلاء ربكما تكذبان﴾ [الرَّحمٰن: 42]
| Khaled Ibrahim Betala “((Inu zolengedwa za mitundu iwiri, anthu ndi ziwanda), kodi ndi mtendere uti wa Mbuye wanu umene mukuukana (kuti si Wake) |