Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rahman ayat 41 - الرَّحمٰن - Page - Juz 27
﴿يُعۡرَفُ ٱلۡمُجۡرِمُونَ بِسِيمَٰهُمۡ فَيُؤۡخَذُ بِٱلنَّوَٰصِي وَٱلۡأَقۡدَامِ ﴾
[الرَّحمٰن: 41]
﴿يعرف المجرمون بسيماهم فيؤخذ بالنواصي والأقدام﴾ [الرَّحمٰن: 41]
Khaled Ibrahim Betala “Adzadziwika oipa (pakati pa anthu ndi ziwanda) ndi zizindikiro zawo (zowazindikiritsa). Ndipo adzagwidwa maliombo awo ndi mapazi awo (ndi kuponyedwa ku Jahena) |