Quran with Chichewa translation - Surah An-Nazi‘at ayat 5 - النَّازعَات - Page - Juz 30
﴿فَٱلۡمُدَبِّرَٰتِ أَمۡرٗا ﴾
[النَّازعَات: 5]
﴿فالمدبرات أمرا﴾ [النَّازعَات: 5]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi iwo (angelo) amene akulongosola malamulo (Ake). (Ndithudi inu anthu mudzauka kwa akufa) |