Quran with Chichewa translation - Surah An-Nazi‘at ayat 6 - النَّازعَات - Page - Juz 30
﴿يَوۡمَ تَرۡجُفُ ٱلرَّاجِفَةُ ﴾ 
[النَّازعَات: 6]
﴿يوم ترجف الراجفة﴾ [النَّازعَات: 6]
| Khaled Ibrahim Betala “Patsiku lomwe (lipenga loyamba lidzaimbidwa), dziko lapansi ndi mapiri ake zidzagwedezeka (ndipo aliyense adzafa) |