Quran with Chichewa translation - Surah At-Takwir ayat 10 - التَّكوير - Page - Juz 30
﴿وَإِذَا ٱلصُّحُفُ نُشِرَتۡ ﴾
[التَّكوير: 10]
﴿وإذا الصحف نشرت﴾ [التَّكوير: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi pamene makalata (momwe mudalembedwa zochita za aliyense) adzatambasulidwe ndi kugawidwa (kuti awerengedwe) |