Quran with Chichewa translation - Surah At-Takwir ayat 24 - التَّكوير - Page - Juz 30
﴿وَمَا هُوَ عَلَى ٱلۡغَيۡبِ بِضَنِينٖ ﴾
[التَّكوير: 24]
﴿وما هو على الغيب بضنين﴾ [التَّكوير: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sali iye (Mtumiki) waumbombo ndi chivumbulutso (koma amafikitsa zonse ndi kuziphunzitsa kwa anthu) |