Quran with Chichewa translation - Surah At-Takwir ayat 5 - التَّكوير - Page - Juz 30
﴿وَإِذَا ٱلۡوُحُوشُ حُشِرَتۡ ﴾
[التَّكوير: 5]
﴿وإذا الوحوش حشرت﴾ [التَّكوير: 5]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi pamene nyama za mtchire zidzasonkhanitsidwe pamodzi (kuchokera mmalo osiyanasiyana chifukwa chakuopsa kwakukulu kwa tsikulo) |