Quran with Chichewa translation - Surah Al-Buruj ayat 22 - البُرُوج - Page - Juz 30
﴿فِي لَوۡحٖ مَّحۡفُوظِۭ ﴾
[البُرُوج: 22]
﴿في لوح محفوظ﴾ [البُرُوج: 22]
Khaled Ibrahim Betala “Yomwe idachokera mu ubawo (chisileti chachikulu) wotetezedwa (ndi manja alionse, osintha kanthu kapena kuonjezerapo) |