Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zalzalah ayat 8 - الزَّلزَلة - Page - Juz 30
﴿وَمَن يَعۡمَلۡ مِثۡقَالَ ذَرَّةٖ شَرّٗا يَرَهُۥ ﴾
[الزَّلزَلة: 8]
﴿ومن يعمل مثقال ذرة شرا يره﴾ [الزَّلزَلة: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene angachite choipa cholemera ngati kanjere kakang’ono, adzaona malipiro ake. (Allah sachitira chinyengo aliyense) |