Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 88 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَقَالُواْ ٱتَّخَذَ ٱلرَّحۡمَٰنُ وَلَدٗا ﴾
[مَريَم: 88]
﴿وقالوا اتخذ الرحمن ولدا﴾ [مَريَم: 88]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (osakhulupirira omwe ndi Ayuda ndi Akhirisitu) akuti: “(Allah) Mwini chifundo chambiri wadzipangira mwana!” |