×

Ndipo iwo amene ali ndi chikhulupiriro ndipo amachita ntchito zabwino, iwo ndi 2:82 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:82) ayat 82 in Chichewa

2:82 Surah Al-Baqarah ayat 82 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 82 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ أُوْلَٰٓئِكَ أَصۡحَٰبُ ٱلۡجَنَّةِۖ هُمۡ فِيهَا خَٰلِدُونَ ﴾
[البَقَرَة: 82]

Ndipo iwo amene ali ndi chikhulupiriro ndipo amachita ntchito zabwino, iwo ndi eni ake a Paradiso ndipo adzakhala komweko mpaka kale kale

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين آمنوا وعملوا الصالحات أولئك أصحاب الجنة هم فيها خالدون, باللغة نيانجا

﴿والذين آمنوا وعملوا الصالحات أولئك أصحاب الجنة هم فيها خالدون﴾ [البَقَرَة: 82]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akhulupirira nachita zabwino, iwowo ndiwo anthu a ku Munda wamtendere. M’menemo adzakhala nthawi yaitali
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek