Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 8 - طه - Page - Juz 16
﴿ٱللَّهُ لَآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَۖ لَهُ ٱلۡأَسۡمَآءُ ٱلۡحُسۡنَىٰ ﴾ 
[طه: 8]
﴿الله لا إله إلا هو له الأسماء الحسنى﴾ [طه: 8]
| Khaled Ibrahim Betala “Allah! Palibe wopembedzedwa mwachoonadi koma Iye. Iye ali ndi maina abwino (ndi mbiri zabwinonso) |