Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 7 - طه - Page - Juz 16
﴿وَإِن تَجۡهَرۡ بِٱلۡقَوۡلِ فَإِنَّهُۥ يَعۡلَمُ ٱلسِّرَّ وَأَخۡفَى ﴾
[طه: 7]
﴿وإن تجهر بالقول فإنه يعلم السر وأخفى﴾ [طه: 7]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati ulankhula mokweza mawu, (iwe munthu), ndithu Iye akudziwa zobisika ndi zobisika kwambiri (zomwe mwazibisa mu mtima mwanu) |